Genesis 46:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Anthu onse amʼnyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+
27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Anthu onse amʼnyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+