Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Chifukwa ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+

  • Deuteronomo 29:10-13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli, 11 ana anu, akazi anu,+ mlendo+ amene akukhala mumsasa wanu, kuyambira amene amakutolerani nkhuni mpaka amene amakutungirani madzi. 12 Inu muli pano kuti mulumbire nʼkuchita pangano ndi Yehova Mulungu wanu, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+ 13 Cholinga chake nʼchakuti lero akupangeni kuti mukhale anthu ake+ komanso kuti iye akhale Mulungu wanu,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani ndiponso mogwirizana ndi zimene analumbira kwa makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena