Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chifukwa ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, pa anthu onse okhala padziko lapansi.+

  • Deuteronomo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Mukamveradi mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero, Yehova Mulungu wanu adzakukwezani ndithu pamwamba pa mitundu yonse ya padziko lapansi.+

  • Deuteronomo 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova adzakupangani kukhala anthu ake oyera,+ mogwirizana ndi zimene analumbira kwa inu,+ chifukwa mukupitiriza kusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu ndipo mukuyenda mʼnjira zake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena