Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthu adzamva+ ndipo adzanjenjemera.

      Anthu okhala ku Filisitiya adzamva ululu.*

  • Ekisodo 23:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Inu musanafike, ndidzawachititsa kuti azindiopa.+ Ndidzasokoneza anthu onse amene mudzakumane nawo. Ndipo ndidzachititsa kuti adani anu onse agonje nʼkuthawa.*+

  • Deuteronomo 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Palibe munthu amene adzalimbane nanu.+ Yehova Mulungu wanu adzachititsa dziko lonse limene mudzayendemo kugwidwa ndi mantha aakulu ndipo adzakuopani,+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.

  • Yoswa 2:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo anawauza kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani dzikoli+ ndipo tonse tikuchita nanu mantha.+ Aliyense mʼdzikoli mtima wake suli mʼmalo chifukwa cha inu.+ 10 Tinamva mmene Yehova anaphwetsera madzi a Nyanja Yofiira pamene munkachoka ku Iguputo.+ Komanso mmene munaphera mafumu awiri a Aamori, Sihoni+ ndi Ogi,+ kutsidya* kwa mtsinje wa Yorodano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena