Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake.

  • Miyambo 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa munthu,+

      Ndipo popereka madalitsowa Mulungu sawonjezerapo ululu.*

  • Yesaya 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mukakhala ndi mtima wofuna kundimvera,

      Mudzadya zinthu zabwino za mʼdziko lanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena