Maliro 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maso anga atopa ndi kugwetsa misozi.+ Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Chiwindi changa chakhuthulidwa pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda akukomoka mʼmabwalo a mzinda.+ Maliro 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda. Khuthula mtima wako pamaso pa Yehova ngati madzi. Pemphera utakweza manja ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala pamphambano za misewu yonse.+ Maliro 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+
11 Maso anga atopa ndi kugwetsa misozi.+ Mʼmimba mwanga mukubwadamuka. Chiwindi changa chakhuthulidwa pansi chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga,+Ndiponso chifukwa chakuti ana ndi makanda akukomoka mʼmabwalo a mzinda.+
19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda. Khuthula mtima wako pamaso pa Yehova ngati madzi. Pemphera utakweza manja ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala pamphambano za misewu yonse.+
10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+