Levitiko 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzabweretsa lupanga lobwezera chilango pa inu chifukwa chophwanya pangano.+ Mukadzathawira mʼmizinda yanu, ndidzabweretsa matenda pakati panu+ ndipo mudzaperekedwa mʼdzanja la mdani.+ Yeremiya 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala ndi mliri,*+ mpaka adzatheratu mʼdziko limene ndinapereka kwa iwowo ndi makolo awo.”’”
25 Ndidzabweretsa lupanga lobwezera chilango pa inu chifukwa chophwanya pangano.+ Mukadzathawira mʼmizinda yanu, ndidzabweretsa matenda pakati panu+ ndipo mudzaperekedwa mʼdzanja la mdani.+
10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala ndi mliri,*+ mpaka adzatheratu mʼdziko limene ndinapereka kwa iwowo ndi makolo awo.”’”