Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.*

  • Deuteronomo 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mukatero mkwiyo wa Yehova udzakuyakirani ndipo iye adzatseka kumwamba moti mvula sidzagwa+ komanso nthaka sidzapereka zokolola zake. Zikadzatero mudzatha mofulumira mʼdziko labwino limene Yehova akukupatsani.+

  • 1 Mafumu 17:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Eliya*+ wa ku Tisibe, wochokera ku Giliyadi anauza Ahabu+ kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wa Isiraeli amene ndimamʼtumikira, sikubwera mame kapena mvula zaka zikubwerazi, pokhapokha ine nditanena.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena