Levitiko 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ngati simudzandimvera kapena kutsatira malamulo onsewa,+ Levitiko 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+ 1 Samueli 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Afilisiti anamenyadi nkhondo ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense anathawira kutenti yake. Aisiraeli amene anaphedwa anali ambiri. Panaphedwa asilikali oyenda pansi okwana 30,000.
17 Ine ndidzakukanani, ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+
10 Choncho Afilisiti anamenyadi nkhondo ndipo Aisiraeli anagonja+ moti aliyense anathawira kutenti yake. Aisiraeli amene anaphedwa anali ambiri. Panaphedwa asilikali oyenda pansi okwana 30,000.