Yeremiya 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ndidzakuchotsani mʼdziko lino nʼkukupititsani kudziko limene inu kapena makolo anu sankalidziwa.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina masana ndi usiku+ chifukwa sindidzakuchitirani chifundo.”’
13 Choncho ndidzakuchotsani mʼdziko lino nʼkukupititsani kudziko limene inu kapena makolo anu sankalidziwa.+ Kumeneko mukatumikira milungu ina masana ndi usiku+ chifukwa sindidzakuchitirani chifundo.”’