2 Mafumu 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno mfumuyo inamʼfunsa kuti: “Chavuta nʼchiyani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero ndipo mawa tidzadya mwana wanga.’+ Maliro 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+
28 Ndiyeno mfumuyo inamʼfunsa kuti: “Chavuta nʼchiyani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero ndipo mawa tidzadya mwana wanga.’+
10 Azimayi amene amakhala achifundo, aphika ana awo ndi manja awo.+ Anawo akhala chakudya chawo pa nthawi yachisoni pamene mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+
10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+