Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+ Nehemiya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chonde, kumbukirani mawu amene munauza* mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+ Luka 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu mpaka nthawi zoikidwiratu za anthu a mitundu inawo zitakwanira.+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+
8 Chonde, kumbukirani mawu amene munauza* mtumiki wanu Mose kuti, ‘Mukadzachita zinthu mosakhulupirika, ndidzakumwazani pakati pa anthu a mitundu ina.+
24 Anthu adzaphedwa ndi lupanga ndiponso kutengedwa ukapolo kupita nawo ku mitundu ina yonse.+ Anthu a mitundu ina adzapondaponda Yerusalemu mpaka nthawi zoikidwiratu za anthu a mitundu inawo zitakwanira.+