Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chifukwa mngelo wanga adzakutsogolerani nʼkukulowetsani mʼdziko la Aamori, Ahiti, Aperezi, Akanani, Ahivi ndi Ayebusi ndipo ine ndidzawawononga.+

  • Numeri 22:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndiyeno buluyo ataona mngelo wa Yehova ataima pamsewu lupanga lake lili mʼmanja, anayesa kuchoka mumsewu nʼkupatukira kutchire. Koma Balamu anayamba kumʼkwapula kuti abwerere mumsewu.

  • 1 Mbiri 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Davide atakweza maso, anaona mngelo wa Yehova ataima mʼmalere* atagwira lupanga+ nʼkuloza Yerusalemu ndi lupangalo. Davide ndi akulu amene anali naye anali atavala ziguduli+ ndipo nthawi yomweyo, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo kufika pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena