Ekisodo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+ 1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+ Danieli 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya ananditsekereza kwa masiku 21. Ndiyeno Mikayeli,*+ mmodzi wa akalonga aakulu,* anabwera kudzandithandiza. Pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pomwepo pafupi ndi mafumu a Perisiya.
20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+
19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+
13 Koma kalonga+ wa ufumu wa Perisiya ananditsekereza kwa masiku 21. Ndiyeno Mikayeli,*+ mmodzi wa akalonga aakulu,* anabwera kudzandithandiza. Pa nthawi imeneyo ndinakhalabe pomwepo pafupi ndi mafumu a Perisiya.