-
Oweruza 3:1-3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yehova analola mitundu yotsatirayi kukhalabe mʼdzikoli nʼcholinga choti ayese Aisiraeli onse amene anali asanaonepo nkhondo zimene mtunduwo unamenya ku Kanani.+ 2 (Anachita zimenezi kuti mibadwo ya Aisiraeli imene sinaonepo nkhondo, iphunzire ndi kudziwa kumenya nkhondo.) 3 Mitundu yake inali olamulira 5 a Afilisiti,+ Akanani onse, Asidoni+ komanso Ahivi+ okhala mʼphiri la Lebanoni,+ kuchokera kuphiri la Baala-herimoni mpaka ku Lebo-hamati.*+
-