Yoswa 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo. Oweruza 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mwamunayo sanavomere kuti agonenso. Choncho ananyamuka ndipo anayenda mpaka kukafika pafupi ndi Yebusi yemwenso ndi Yerusalemu.+ Pa ulendowu anali ndi abulu awiri aja, okhala ndi zishalo ndipo analinso ndi mkazi wake komanso mtumiki wake.
28 Zela,+ Ha-elefi, Yebusi, kutanthauza Yerusalemu,+ Gibea+ ndi Kiriyati. Mizinda 14 ndi midzi yake. Chimenechi chinali cholowa cha ana a Benjamini motsatira mabanja awo.
10 Koma mwamunayo sanavomere kuti agonenso. Choncho ananyamuka ndipo anayenda mpaka kukafika pafupi ndi Yebusi yemwenso ndi Yerusalemu.+ Pa ulendowu anali ndi abulu awiri aja, okhala ndi zishalo ndipo analinso ndi mkazi wake komanso mtumiki wake.