Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Beti-semesi ndi malo ake odyetserako ziweto. Panali mizinda 9 kuchokera mʼmafuko awiri amenewa.
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
16 Aini+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Yuta+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Beti-semesi ndi malo ake odyetserako ziweto. Panali mizinda 9 kuchokera mʼmafuko awiri amenewa.