Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Eloni, Timuna,+ Ekironi,+

  • Yoswa 19:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ichi chinali cholowa cha fuko la Dani motsatira mabanja awo, ndipo imeneyi inali mizinda yawo ndi midzi yake.

  • Oweruza 14:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako Samisoni anapita ku Timuna ndipo kumeneko anaona mkazi wa Chifilisiti. 2 Choncho anakauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ndaona mkazi wa Chifilisiti wokongola ku Timuna, ndiye mukanditengere kuti akhale mkazi wanga.”

  • 2 Mbiri 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nawonso Afilisiti+ anaukira mizinda ya Yuda ya ku Sefela+ ndi ku Negebu nʼkulanda mzinda wa Beti-semesi,+ wa Aijaloni+ ndi wa Gederoti. Analandanso mzinda wa Soko ndi midzi yake yozungulira, Timuna+ ndi midzi yake yozungulira komanso wa Gimizo ndi midzi yake yozungulira, ndipo anayamba kukhala kumeneko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena