Numeri 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tinaonakonso Anefili,* ana a Anaki+ omwe ndi mbadwa za Anefili, moti tikadziyerekezera ndi iwowo, ifeyo timangooneka ngati tiziwala. Iwonso ndi mmene amationera.” Yoswa 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa nthawiyo Yoswa anapita nʼkukapha Aanaki+ onse kudera lamapiri, ku Heburoni, ku Debiri, ku Anabi, kudera lonse lamapiri la Yuda ndiponso kudera lonse lamapiri la Isiraeli. Yoswa anapha Aanaki onsewo nʼkuwononga mizinda yawo.+
33 Tinaonakonso Anefili,* ana a Anaki+ omwe ndi mbadwa za Anefili, moti tikadziyerekezera ndi iwowo, ifeyo timangooneka ngati tiziwala. Iwonso ndi mmene amationera.”
21 Pa nthawiyo Yoswa anapita nʼkukapha Aanaki+ onse kudera lamapiri, ku Heburoni, ku Debiri, ku Anabi, kudera lonse lamapiri la Yuda ndiponso kudera lonse lamapiri la Isiraeli. Yoswa anapha Aanaki onsewo nʼkuwononga mizinda yawo.+