Yoswa 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ Yoswa 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chinalinso Aini, Rimoni, Eteri ndi Asani.+ Mizinda 4 ndi midzi yake Nehemiya 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ayuda ena ankakhala mʼmidzi ndi mʼmadera ozungulira midziyo. Ena ankakhala ku Kiriyati-ariba+ ndi midzi yake yozungulira, ku Diboni ndi midzi yake yozungulira, ku Yekabizeeli+ ndi midzi yake yozungulira, Nehemiya 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ku Eni-rimoni,+ ku Zora,+ ku Yarimuti,
19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+
25 Ayuda ena ankakhala mʼmidzi ndi mʼmadera ozungulira midziyo. Ena ankakhala ku Kiriyati-ariba+ ndi midzi yake yozungulira, ku Diboni ndi midzi yake yozungulira, ku Yekabizeeli+ ndi midzi yake yozungulira,