Yoswa 19:40, 41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Maere a 7+ anagwera fuko la Dani+ motsatira mabanja awo. 41 Malire a gawo la cholowa chawo anadutsa ku Zora,+ Esitaoli, Iri-semesi, Oweruza 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako azichimwene ake ndi anthu onse akubanja la bambo ake, anapita kukatenga mtembo wa Samisoni nʼkudzauika mʼmanda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli. Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+
40 Maere a 7+ anagwera fuko la Dani+ motsatira mabanja awo. 41 Malire a gawo la cholowa chawo anadutsa ku Zora,+ Esitaoli, Iri-semesi,
31 Kenako azichimwene ake ndi anthu onse akubanja la bambo ake, anapita kukatenga mtembo wa Samisoni nʼkudzauika mʼmanda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli. Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+