Yoswa 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+ Yoswa 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chinalinso Aini, Rimoni, Eteri ndi Asani.+ Mizinda 4 ndi midzi yake
19 Maere achiwiri+ anagwera Simiyoni, kutanthauza fuko la Simiyoni,+ motsatira mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha Yuda.+