Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yatiri+ ndi malo ake odyetserako ziweto, Esitemowa+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+