Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma patapita masiku atatu atachita nawo panganolo, anamva kuti anthuwo ankakhala pafupi, mʼdera lomwelo. 17 Aisiraeliwo ananyamuka nʼkukafika kumizinda ya anthuwo pa tsiku lachitatu. Mizindayo inali Gibiyoni,+ Kefira, Beeroti ndi Kiriyati-yearimu.+

  • Yoswa 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Maere oyamba anagwera fuko la Benjamini motsatira mabanja awo, ndipo anapatsidwa dera limene linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+

  • Yoswa 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kumadzulo kwa gawolo, malirewo anakhotera kumʼmwera, paphiri loyangʼanizana ndi kumʼmwera kwa Beti-horoni. Kuchokera pamenepo anakathera ku Kiriyati-baala, kutanthauza Kiriyati-yearimu,+ womwe ndi mzinda wa Yuda. Amenewa ndi malire akumadzulo a gawo la Benjamini.

  • 1 Samueli 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho amuna a ku Kiriyati-yearimu anabweradi nʼkutenga Likasa la Yehova ndipo anakaliika mʼnyumba ya Abinadabu+ imene inali paphiri. Ndiyeno anasankha* Eliezara mwana wake kuti azilondera Likasa la Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena