Genesis 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yosefe+ ndi mphukira yamtengo wobala zipatso. Iye ndi mtengo wobala zipatso pakasupe, umene nthambi zake zimafika pamwamba pa khoma la mpanda. Deuteronomo 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponena za Yosefe anati:+ “Dziko lake lidalitsidwe ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba,Ndi mame komanso madzi ochokera mu akasupe a pansi pa nthaka.+
22 Yosefe+ ndi mphukira yamtengo wobala zipatso. Iye ndi mtengo wobala zipatso pakasupe, umene nthambi zake zimafika pamwamba pa khoma la mpanda.
13 Ponena za Yosefe anati:+ “Dziko lake lidalitsidwe ndi Yehova.+Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri zakumwamba,Ndi mame komanso madzi ochokera mu akasupe a pansi pa nthaka.+