2 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kumapeto kwa zaka 20 zimene Solomo anamanga nyumba ya Yehova ndiponso nyumba* yake,+ 2 Mbiri 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anamanganso mzinda wa Beti-horoni+ Wakumtunda ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, mageti ndi mipiringidzo.
5 Anamanganso mzinda wa Beti-horoni+ Wakumtunda ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, mageti ndi mipiringidzo.