Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 17:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako ana a Yosefe anati: “Dera lamapiri silitikwanira, ndiponso Akanani akuchigwa, a ku Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira ndiponso akuchigwa cha Yezereeli+ ali ndi magaleta ankhondo+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa.”

  • Oweruza 6:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa anasonkhanitsa asilikali awo+ ndipo anawoloka mtsinje nʼkukamanga msasa mʼchigwa cha Yezereeli.

  • 1 Mafumu 21:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako panachitika nkhani yokhudza munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli. Mundawu unali ku Yezereeli,+ pafupi ndi nyumba yachifumu ya Ahabu mfumu ya Samariya.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena