1 Samueli 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+ 1 Mafumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anafufuza mtsikana wokongola mʼdziko lonse la Isiraeli. Kenako anapeza Abisagi+ wa ku Sunemu+ ndipo anabwera naye kwa mfumu. 2 Mafumu 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza Elisa kuti adye chakudya.+ Nthawi zonse Elisa akamadutsa, ankaima kunyumba kwa mayiyo kuti adye chakudya.
4 Afilisiti anasonkhana nʼkukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse nʼkukamanga msasa ku Giliboa.+
3 Ndiyeno anafufuza mtsikana wokongola mʼdziko lonse la Isiraeli. Kenako anapeza Abisagi+ wa ku Sunemu+ ndipo anabwera naye kwa mfumu.
8 Tsiku lina Elisa anapita ku Sunemu.+ Kumeneko kunali mayi wina wodziwika. Mayiyo anaumiriza Elisa kuti adye chakudya.+ Nthawi zonse Elisa akamadutsa, ankaima kunyumba kwa mayiyo kuti adye chakudya.