Numeri 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma dzikolo uligawe pochita maere.+ Onse alandire cholowa chawo potengera mayina a mafuko a makolo awo. Yoswa 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma inuyo mukagawe dzikolo mʼzigawo 7 ndipo mukazilembe. Kenako mukabwere nazo kuno kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.
55 Koma dzikolo uligawe pochita maere.+ Onse alandire cholowa chawo potengera mayina a mafuko a makolo awo.
6 Koma inuyo mukagawe dzikolo mʼzigawo 7 ndipo mukazilembe. Kenako mukabwere nazo kuno kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.