Yoswa 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+ Yoswa 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Aijaloni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.
8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
24 Aijaloni+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda 4.