Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yona 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Yona ananyamuka nʼkulowera ku Tarisi, kuthawa Yehova. Atafika ku Yopa anapeza chombo chopita ku Tarisi. Iye analipira ndalama za ulendowo pothawa Yehova nʼkukwera chombocho kuti apite ku Tarisi limodzi ndi anthu amene anali mmenemo.

  • Machitidwe 9:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Ku Yopa kunali wophunzira wina dzina lake Tabita, dzina limene limamasuliridwa kuti Dorika.* Tabita ankachita zinthu zambiri zabwino ndiponso ankapatsa ena mphatso zambiri zachifundo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena