Numeri 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mizindayo ikakhale malo amene munthu wopha mnzake, amene akuthawa wobwezera magazi+ azikathawirako, kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe mpaka mlandu wake utaweruzidwa pamaso pa oweruza.+ Numeri 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 oweruza aweruze pakati pa wopha mnzakeyo ndi woyenera kubwezera magaziyo, mogwirizana ndi malamulo amenewa.+
12 Mizindayo ikakhale malo amene munthu wopha mnzake, amene akuthawa wobwezera magazi+ azikathawirako, kuti amene wapha mnzakeyo asaphedwe mpaka mlandu wake utaweruzidwa pamaso pa oweruza.+
24 oweruza aweruze pakati pa wopha mnzakeyo ndi woyenera kubwezera magaziyo, mogwirizana ndi malamulo amenewa.+