Numeri 35:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wopha munthuyo ayenera kukhala mumzinda wothawirako mpaka mkulu wa ansembe atamwalira. Pambuyo pa imfa ya mkulu wa ansembe, wopha munthuyo akhoza kubwerera kumalo a cholowa chake.+
28 Wopha munthuyo ayenera kukhala mumzinda wothawirako mpaka mkulu wa ansembe atamwalira. Pambuyo pa imfa ya mkulu wa ansembe, wopha munthuyo akhoza kubwerera kumalo a cholowa chake.+