Yoswa 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Poyamba mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba.+ (Ariba anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki.) Kenako mʼdzikolo munakhala mopanda nkhondo.+ Yoswa 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a wansembe Aroni anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake,+ wa Heburoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
15 Poyamba mzinda wa Heburoni unkatchedwa Kiriyati-ariba.+ (Ariba anali munthu wamphamvu pakati pa Aanaki.) Kenako mʼdzikolo munakhala mopanda nkhondo.+
13 Ana a wansembe Aroni anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake,+ wa Heburoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Libina+ ndi malo ake odyetserako ziweto,