-
1 Mbiri 6:77, 78Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa anthu a ku banja la Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto. 78 Kuchokera ku fuko la Rubeni, anawapatsa mzinda wa Bezeri mʼchipululu ndi malo ake odyetserako ziweto. Mzindawo unali mʼchigawo cha Yorodano pafupi ndi Yeriko chakumʼmawa kwa Yorodano. Anawapatsanso mzinda wa Yahazi+ ndi malo ake odyetserako ziweto,
-