Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 21:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho Aisiraeli anachita maere nʼkupatsa Alevi mizinda imeneyi ndi malo ake odyetserako ziweto, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+

  • Yoswa 21:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Kuchokera mʼfuko la Gadi,+ anawapatsa mzinda wothawirako munthu amene wapha mnzake, wa Ramoti ku Giliyadi+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,

  • 1 Mbiri 6:77
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 77 Kuchokera ku fuko la Zebuloni,+ anapatsa anthu a ku banja la Merari amene anatsala, mzinda wa Rimono ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Tabori ndi malo ake odyetserako ziweto.

  • 1 Mbiri 6:80
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 80 Kuchokera ku fuko la Gadi, anawapatsa mzinda wa Ramoti ku Giliyadi ndi malo ake odyetserako ziweto, mzinda wa Mahanaimu+ ndi malo ake odyetserako ziweto,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena