5 Ansembe, omwe ndi Alevi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti azimutumikira+ komanso azidalitsa mʼdzina la Yehova.+ Iwo ndi amene akuyenera kunena njira yothetsera mkangano uliwonse wokhudza zinthu zankhanza zimene zachitika.+