Ekisodo 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+ Yoswa 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo mʼmanja mwathu.+ Ndipo anthu onse a mʼdzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+
15 Pa nthawi imeneyo mafumu a ku Edomu adzachita mantha.Ndipo olamulira amphamvu a ku Mowabu adzanjenjemera.+ Anthu onse okhala mu Kanani adzataya mtima.+
24 Iwo anauza Yoswa kuti: “Yehova wapereka dziko lonselo mʼmanja mwathu.+ Ndipo anthu onse a mʼdzikomo akuchita mantha chifukwa cha ife.”+