Deuteronomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma samalani ndipo mukhale tcheru* kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona, komanso kuti zinthu zimenezo zisachoke mumtima mwanu masiku onse a moyo wanu. Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauzanso zinthu zimenezo.+ Salimo 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.
9 Koma samalani ndipo mukhale tcheru* kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona, komanso kuti zinthu zimenezo zisachoke mumtima mwanu masiku onse a moyo wanu. Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauzanso zinthu zimenezo.+
44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita mu nthawi yawo,Mʼmasiku akale.