Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno anati: “Yehova, ngati mungandikomere mtima, chonde, musangondipitirira ine mtumiki wanu.

  • Genesis 18:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Popeza mwafika kwa mtumiki wanu, ndiloleni ndikubweretsereni kachakudya kuti mupezenso mphamvu. Kenako mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”

  • Oweruza 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano Manowa anauza mngelo wa Yehova kuti: “Dikirani pangʼono tikukonzereni kamwana ka mbuzi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena