Danieli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,*+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu limba mtima.” Akulankhula nane, ndinalimbikitsidwa ndipo ndinanena kuti: “Lankhulani mbuyanga chifukwa inu mwandilimbikitsa.”
19 Kenako anandiuza kuti: “Iwe munthu wokondedwa kwambiri,*+ usachite mantha.+ Mtendere ukhale nawe.+ Limba mtima, ndithu limba mtima.” Akulankhula nane, ndinalimbikitsidwa ndipo ndinanena kuti: “Lankhulani mbuyanga chifukwa inu mwandilimbikitsa.”