Oweruza 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa anasonkhanitsa asilikali awo+ ndipo anawoloka mtsinje nʼkukamanga msasa mʼchigwa cha Yezereeli.
33 Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa anasonkhanitsa asilikali awo+ ndipo anawoloka mtsinje nʼkukamanga msasa mʼchigwa cha Yezereeli.