Oweruza 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma Yehova anamuuza kuti: “Chifukwa ndidzakhala nawe,+ udzapha Amidiyani ngati ukupha munthu mmodzi.”
16 Koma Yehova anamuuza kuti: “Chifukwa ndidzakhala nawe,+ udzapha Amidiyani ngati ukupha munthu mmodzi.”