Oweruza 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero, Yehova anamuyangʼana nʼkumuuza kuti: “Pita ndi mphamvu zimene uli nazozi, ndipo udzapulumutsa Isiraeli kwa Amidiyani.+ Kodi si ine amene ndakutuma?”
14 Atatero, Yehova anamuyangʼana nʼkumuuza kuti: “Pita ndi mphamvu zimene uli nazozi, ndipo udzapulumutsa Isiraeli kwa Amidiyani.+ Kodi si ine amene ndakutuma?”