Oweruza 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa mʼmagulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo mʼmitsukomo anaikamo zounikira.
16 Ndiyeno amuna 300 aja anawagawa mʼmagulu atatu. Aliyense anamupatsa lipenga la nyanga ya nkhosa+ ndi mtsuko waukulu wopanda kanthu, ndipo mʼmitsukomo anaikamo zounikira.