-
Oweruza 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako Gidiyoni anafika ku Yorodano nʼkuwoloka mtsinjewo pamodzi ndi amuna 300 amene anali nawo aja. Anali atatopa koma ankathamangitsabe adaniwo.
-