Ekisodo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Apange efodi wopeta ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Oweruza 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mika anali ndi nyumba ya milungu ndipo anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake udindo woti akhale wansembe wake.+
6 Apange efodi wopeta ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+
5 Mika anali ndi nyumba ya milungu ndipo anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake udindo woti akhale wansembe wake.+