Oweruza 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Aisiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Choncho Yehova anawapereka mʼmanja mwa Amidiyani kwa zaka 7.+
6 Koma Aisiraeli anayambanso kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Choncho Yehova anawapereka mʼmanja mwa Amidiyani kwa zaka 7.+