2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ataliya,+ mayi ake a Ahaziya ataona kuti mwana wawo wafa,+ anapha anthu onse amene anali oyenera kulowa ufumu.*+ 2 Mbiri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, anapha ndi lupanga azichimwene ake onse+ ndiponso akalonga ena a Isiraeli. Iye anachita zimenezi kuti alimbitse ufumu wake.
11 Ataliya,+ mayi ake a Ahaziya ataona kuti mwana wawo wafa,+ anapha anthu onse amene anali oyenera kulowa ufumu.*+
4 Yehoramu atayamba kulamulira mu ufumu wa bambo ake, anapha ndi lupanga azichimwene ake onse+ ndiponso akalonga ena a Isiraeli. Iye anachita zimenezi kuti alimbitse ufumu wake.