Deuteronomo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani nʼkulitenga kukhala lanu ndipo mukukhalamo, ndiye inu nʼkunena kuti, ‘Tisankhe mfumu ngati mitundu ina yonse imene yatizungulira,’+ 1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+
14 Mukakalowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani nʼkulitenga kukhala lanu ndipo mukukhalamo, ndiye inu nʼkunena kuti, ‘Tisankhe mfumu ngati mitundu ina yonse imene yatizungulira,’+
7 Yehova anauza Samueli kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akuuza, chifukwatu sanakane iwe koma akana ine kuti ndikhale mfumu yawo.+